Mark 15:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atamva mauwo, ena amene adaaimirira pamenepo adati, “Tamverani, akuitana Eliya.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ena akuimirirapo, pakumva, ananena, Taonani, aitana Eliya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ena amene anali pafupi atamva izi anati, “Tamverani, akuyitana Eliya.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ena akuimirirapo, paku mva, ananena, Taonani, aitana Eliya