Mark 15:38 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chinsalu chochinga chija cha m'Nyumba ya Mulungu chidang'ambika pakatimpakati, kuyambira pamwamba mpaka pansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo chinsalu chotchinga cha m'Kachisi chinang'ambika pakati, kuyambira kumwamba kufikira pansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chinsalu chotchinga cha mʼNyumba ya Mulungu chinangʼambika pakati kuyambira pamwamba mpaka pansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo cinsart cocinga ca m'Kacisi cinang'ambika pakati, kuyambira kumwamba kufikira pansi.