Mark 15:45 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mkulu wa asilikaliyo atavomera, Pilato adamlola Yosefe kuti akatenge mtembowo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene anachidziwa ndi kenturiyo, anamninkha Yosefe mtembowo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atawuzidwa ndi Kenturiyo kuti zinali motero, anapereka mtembowo kwa Yosefe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene anacidziwa ndi kenturiyo, anamninkha Yosefe ntembowo.