Mark 15:47 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maria uja wa ku Magadala, ndi Maria mai wa Yosefe, ankaona kumene adamuika Yesu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Maria wa Magadala ndi Maria amake wa Yosefe anapenya pomwe anaikidwapo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mariya Magadalena ndi Mariya amayi a Yose anaona kumene anamuyika Yesu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Maliya wa Magadala ndi Maliya amace wa Yose anapenya pomwe anaikidwapo.