Mark 15:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Panali munthu wina, dzina lake Barabasi, amene anali m'ndende pamodzi ndi anthu ena chifukwa choukira Boma ndi kupha anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo analipo wina dzina lake Barabasi, wamangidwa pamodzi ndi opanduka, amene anapha munthu mumphandumo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu wotchedwa Baraba anali mʼndende pamodzi ndi anthu owukira amene anapha anthu pa nthawi ya chipolowe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo analipo wina dzina lace Baraba, womangidwa pamodzi ndi opanduka, amene anapha munthu mumphandumo.