Mark 15:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono chikhamu cha anthu chidabwera, nkuyamba kupempha Pilato kuti aŵachitire zomwe adaazoloŵera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo khamu la anthu anabwera nayamba kupempha kuti achite monga anali kuwachitira nthawi zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Gulu la anthu linabwera kwa Pilato ndi kumufunsa kuti awachitire zimene amachita nthawi zonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo khamu la anthu anabwera nayamba kupempha kuti acite monga adafuwacitira.