Mark 15:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pilato adaŵafunsa kuti, “Kodi mukufuna kuti ndikumasulireni Mfumu ya Ayudayi?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Pilato anawayankha, nanena nao, Kodi mufuna kuti ndikumasulireni mfumu ya Ayuda?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kodi mukufuna kuti ndikumasulireni mfumu ya Ayuda?” Pilato anafunsa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Pilato anawayankha, nanena nao, Kodi mufuna kuti ndikumasulireni Mfumu ya Ayuda?