Mark 2:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma idzafika nthaŵi pamene adzaŵachotsere mkwatiyo. Pamenepo ndiye azidzasala zakudya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma adzadza masiku, pamene mkwati adzachotsedwa kwa iwo, ndipo pamenepo adzasala kudya tsiku lomwelo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma nthawi idzafika pamene mkwati adzachotsedwa pakati pawo, ndipo pa tsiku limenelo adzasala kudya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma adzadza masiku, pamene mkwati adzacotsedwa kwa iwo, ndipo pamenepo adzasala kudya tsiku lomwelo.