Mark 2:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho Mwana wa Munthu ali ndi ulamuliro wonse pa zokhudza tsiku la Sabata.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
motero Mwana wa Munthu ali mwini tsiku la Sabata lomwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Mwana wa Munthu ali Ambuye ngakhale wa Sabata.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
motero Mwana wa munthu ali mwini dzuwa la Sabata lomwe.