Mark 2:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu ena anai adaanyamula munthu wa ziwalo zakufa, kubwera naye kwa Yesu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anadza kwa Iye otenga munthu wodwala manjenje, wonyamulidwa ndi anthu anai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amuna anayi anabwera, atanyamula munthu wofa ziwalo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anadza kwa Iye otenga munthu wodwala manjenje, wonyamulidwa ndi anthu anai.