Mark 2:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma pamenepo panalinso aphunzitsi ena a Malamulo a Mose. Iwowo adayamba kudzifunsa mumtima mwao kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anakhalapo ena a alembi akuganizira mumtima mwao,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ena mwa aphunzitsi amalamulo anakhala pansi pomwepo, namaganiza mʼmitima mwawo kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anakhalapo ena a alembi akuganizira mumtima mwao,