Mark 2:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Yesu adaadziŵa kuti akuganiza zimenezi mumtima mwao, motero adaŵafunsa kuti, “Bwanji mukuganiza zimenezo mumtima mwanu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pomwepo Yesu pozindikira mumtima mwake kuti alikuganizira chomwecho mwa iwo okha, ananena nao, Muganiza bwanji zinthu izi m'mitima yanu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nthawi yomweyo Yesu anadziwa mu mzimu wake kuti izi ndi zimene ankaganiza mʼmitima yawo, ndipo anawawuza kuti, “Chifukwa chiyani mukuganiza zinthu izi?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pomwepo Yesu pozindikira mumtima mwace kuti alikuganizira comweco mwa iwo okha, ananena nao, Muganiza bwanji zinthu izi m'mitima yanu?