Mark 3:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndipo mudzakhala ndi mphamvu zotulutsira mizimu yoipa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kuti akhale nao ulamuliro wakutulutsa ziwanda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndi kuti akhale ndi ulamuliro wotulutsa ziwanda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kuti akhale nao ulamuliro wakuturutsa ziwanda.