Mark 3:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Achibale ake atamva zimenezi, adabwera kuti adzamtenge, chifukwa ankati, “Wachita misala.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene abale ake anamva, anadza kudzamgwira Iye; pakuti anati adayaluka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu a ku banja lake atamva zimenezi, anapita kuti akamutenga, pakuti ankanena kuti, “Wazungulira mutu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene abale ace anamva, anadza kudzamgwira Iye; pakuti anati adayaruka.