Mark 3:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo anthu a m'banja limodzi akayamba kugaŵikana, banja lotere silingalimbe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo nyumba ikagawanika pa iyo yokha, sikhoza kukhazikika nyumbayo,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati nyumba igawanikana mwa iyo yokha, nyumba imeneyo singathe kuyima.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo nyumba ikagawanika pa iyo yokha, siikhoza kukhazikika nyumbayo,