Mark 3:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amai ake ndi abale ake a Yesu adabwera kunyumbako. Adaima panja, natuma anthu kuti akamuitane.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anadza amake ndi abale ake; naima kunja, namtumira uthenga kumuitana.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo amayi ndi abale ake a Yesu anafika. Atayima kunja, anatuma wina kuti akamuyitane Iye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anadza amace ndi abale ace; naima kunja, namtumira uthenga kumuitana.