Mark 4:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mbeuzo zikacha, munthu uja amatenga mpeni wodulira, pakuti nyengo yokolola yafika.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakutcha zipatso, pamenepo atenga chisenga, pakuti nthawi yakumweta yafika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mbewuyo ikangokhwima, amayimweta chifukwa nthawi yokolola yakwana.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakucha zipatso, pamenepo atumiza zenga, pakuti nthawi yakumweta yafika.