Mark 4:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Uli ngati njere ya mbeu ya mpiru. Pamene aifesa m'nthaka, ndi yaing'ono kwambiri mukaiyerekeza ndi njere zina pansi pano.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati mbeu yampiru, imene ikafesedwa panthaka, ingakhale ichepa ndi mbeu zonse za padziko,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Uli ngati mbewu ya mpiru imene ndi mbewu yayingʼono kwambiri yomwe mumadzala mʼnthaka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati mbeu yampiru, imene ikafesedwapanthaka, ingakhale icepa ndi mbeu zonse za padziko,