Mark 4:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yesu ankaphunzitsa anthu ndi mafanizo ambiri onga ameneŵa, polinganiza ndi nzeru za anthuwo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndi mafanizo otere ambiri analankhula nao mau, monga anakhoza kumva;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi mafanizo ambiri onga awa Yesu anayankhula mawu kwa iwo, monga mmene akanatha kumvetsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndi mafanizo otere ambiri analankhula nao mau, 1 monga anakhoza kumva;