Mark 5:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo iye adadandaulira Yesu kwambiri kuti mizimuyo asaitulutsire kunja kwa dera limenelo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anampempha Iye kwambiri kuti asaitulutsire kunja kwake kwa dziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anamupempha Yesu mobwerezabwereza kuti asazitulutse mʼderalo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anampempha Iye kwambiri kuti asaiturutsire kunja kwace kwa dziko.