Mark 5:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono panali mai wina amene adakhala akuvutika ndi matenda a msambo pa zaka khumi ndi ziŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo munthu wamkazi amene anali ndi nthenda yachidwalire zaka khumi ndi ziwiri,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pomwepo panali mayi amene amadwala nthenda yotaya magazi kwa zaka khumi ndi ziwiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo munthu wamkazi amene anali ndi nthenda yacidwalire zaka khwni ndi ziwiri,