Mark 5:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mumtima mwake ankaganiza kuti, “Ndikangokhudza ngakhale zovala zake zokhazo, ndichira.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ananena iye, Ngati ndikakhudza ngakhale zovala zake ndidzapulumutsidwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
chifukwa anaganiza kuti, “Ngati nditangokhudza mkanjo wake, ndidzachiritsidwa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ananena iye, Ngati ndikakhudza ngakhale zobvala zace ndidzapulumutsidwa.