Mark 5:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Yesu adayang'anayang'ana kuti aone yemwe wachita zimenezo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Iye anaunguzaunguza kumuona iye amene adachita ichi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Yesu anapitirizabe kuyangʼana kuti aone amene anachita zimenezi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Iye anaunguza-unguza kumuona iye amene adacita ici,