Mark 5:37 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono sadalole kuti winanso atsagane naye, koma Petro, ndi Yakobe, ndi Yohane, mbale wa Yakobeyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo sanalole munthu yense kutsagana naye, koma Petro, ndi Yakobo, ndi Yohane mbale wake wa Yakobo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye sanalole munthu wina aliyense kuti amutsatire koma Petro, Yakobo ndi Yohane mʼbale wa Yakobo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo sanalola munthu yense kutsagana naye, koma Petro, ndi Yakobo, ndi Yohane mbale wace wa Yakobo.