Mark 6:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yesu adachoka kumeneko, nakafika kumudzi kwao. Ophunzira ake adatsagana naye.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Iye anatuluka kumeneko; nafika kudziko la kwao; ndipo ophunzira ake anamtsata.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yesu anachoka kumeneko napita ku mudzi kwawo, pamodzi ndi ophunzira ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Iye anaturuka kumeneko; nafika ku dziko la kwao; ndipo ophunzira ace anamtsata.