Mark 6:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo Yohane adaamuuza kuti, “Nkulakwira Malamulo kulanda mkazi wa mbale wanu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Yohane adanena kwa Herode, Si kuloledwa kwa inu kukhala naye mkazi wa mbale wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Yohane ankanena kwa Herode kuti, “Sikololedwa kwa inu kuti mukwatire mkazi wa mʼbale wanu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Yohane adanena kwa Herode, Si kuloledwa kwa inu kukhala naye mkazi wa mbale wanu.