Mark 6:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
chifukwa Herode ankaopa Yohane, podziŵa kuti anali munthu wolungama ndi woyera mtima. Choncho ankamusunga bwino. Ankakonda kumamvetsera mau ake, ngakhale kuti akamumva choncho, ankathedwa nzeru.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti Herode anaopa Yohane, podziwa kuti ali munthu wolungama ndi woyera mtima, ndipo anamsunga iye. Ndipo pamene anamva iye anathedwa nzeru, nakondwa kumva iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
chifukwa Herode anaopa Yohane ndipo anamuteteza, podziwa kuti iye anali munthu wolungama ndi woyera mtima. Herode akamamva Yohane, ankathedwa nzeru; komabe amakonda kumumvetsera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti Herode anaopa Yohane, podziwa kuti ali munthu wolungama ndi woyera mtima, ndipo anamsunga iye. Ndipo pamene anamva iye anathedwa nzeru, oakondwa kumva iye.