Mark 6:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adatsimikiza molumbira kuti, “Chilichonse chomwe uti undipemphe, ndikupatsa ndithu, ngakhale kukudulira dziko langa lino pakati.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anamlumbirira iye, kuti, Chilichonse ukandipempha ndidzakupatsa, kungakhale kukugawira ufumu wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo analonjeza ndi lumbiriro kuti, “Chilichonse chimene upempha ndidzakupatsa, ngakhale theka la ufumu wanga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anamlumbirira iye, kuti, Ciri conse ukandipempha ndidzakupatsa, kungakhale kukugawira ufumu wanga.