Mark 6:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtsikanayo adatuluka nakafunsa mai wake kuti, “Kodi ndikapemphe chiyani?” Mai wakeyo adati “Kapemphe mutu wa Yohane Mbatizi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anatuluka, nati kwa amake, Ndidzapempha chiyani? Ndipo iye anati, Mutu wake wa Yohane Mbatizi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anatuluka nati kwa amayi ake, “Kodi ndikapemphe chiyani?” Iye anamuyankha kuti, “Mutu wa Yohane Mʼbatizi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anaturuka, nati kwa amace, Ndidzapempha ciani? Ndipo iyel anati, Mutu wace wa Yohane Mbatizi.