Mark 6:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo mfumu Herode adamva chisoni kwambiri. Koma chifukwa cha malumbiro ake ndiponso chifukwa cha anthu oitanidwa ku phwando aja, sadafune kuphwanya lonjezo lake kwa mtsikanayo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu inamva chisoni chachikulu; koma chifukwa cha malumbiro ake, ndi cha iwo akukhala pachakudya, sanafune kumkaniza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu inamva chisoni chachikulu, koma chifukwa cha lumbiro lake ndi alendo ake a pa mphwandolo, sanafune kumukaniza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumu inamva cisoni cacikuru; koma cifukwa ca malumbiro ace, ndi ca iwo akukhala pacakudya, sanafuna kumkaniza.