Mark 6:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaika mutu wakewo m'mbale nkubwera nawo, naupereka kwa mtsikana uja, mtsikanayo nkukaupereka kwa mai wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
natengera mutu wake mumbale, naupereka kwa buthulo; ndipo buthu linaupereka kwa amake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
nabweretsa mutuwo mʼmbale. Anawupereka kwa mtsikanayo, ndipo iye anakapereka kwa amayi ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
natengera mutu wace mumbizi, naupereka kwa buthulo; ndipo buthu linaupereka kwa amace.