Mark 6:36 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Auzeni anthuŵa azipita, anke ku midzi ili pafupiyi kuti azikagula chakudya.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
muwauze kuti amuke, alowe kumilaga ndi kumidzi yozungulira, akadzigulire okha kanthu kakudya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Awuzeni anthuwa azipita ku midzi ndi madera ozungulira, kuti akadzigulire kanthu kakuti adye.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
muwauze kuti amuke, alowe kumiraga ndi ku midzi yozungulira, akadzigulire okha kanthu kakudya.