Mark 6:47 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'mene kunkayamba kuda, nkuti chombo chija chili pakati pa nyanja, Yesu ali yekha pa mtunda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pofika madzulo ngalawa inali pakati pa nyanja, ndi Iye yekha pamtunda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pofika madzulo, bwato linali pakati pa nyanja, ndipo Iye anali yekha pa mtunda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pofika madzulo ngalawa inali pakati pa nyanja, ndi Iye yekha pamtunda.