Mark 6:49 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ophunzira aja, pomuwona akuyenda pa madzi, adaaganiza kuti ndi mzukwa, nayamba kukuwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma iwo, pamene anamuona alikuyenda panyanja, anayesa kuti ndi mzukwa, nafuula:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
koma atamuona Iye akuyenda pa nyanja, anaganiza kuti anali mzukwa. Iwo anafuwula,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma iwo, pamene anamuona alikuyenda panyanja, anayesa kuti ndi mzukwa, napfuula: