Mark 6:52 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
chifukwa anali asanamvetse bwino za buledi zija. Mitu yao idaali youma.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti sanazindikire za mikateyo, koma mitima yao inauma.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
popeza sanazindikire zimene zinachitika pa malofu a buledi; pakuti mitima yawo inali yowuma.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti sanazindikira za mikateyo, kama mitima yao inauma.