Mark 6:55 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adathamangira ku midzi ya kufupi ndi kumeneko, nayamba kumabwera ndi anthu odwala pa machira, kudza nawo kumene ankamva kuti Yesu ali uku.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nathamangira dziko lonselo nayamba kunyamula anthu odwala pa mphasa zao, kufika nao kumene anamva kuti analiko Iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anathamanga uku ndi uko mʼdera lonse nakanyamula odwala pa machira kupita nawo kulikonse kumene anamva kuti kuli Iye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nathamangira dziko lonselo nayamba kunyamula anthu odwaia pa akama ao, kufika nao kumene anamva kuti analiko Iye.