Mark 7:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Yesu adasiya khamu lija la anthu nakaloŵa m'nyumba, ophunzira ake adamufunsa za fanizo limeneli.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo m'mene Iye adalowa m'nyumba kusiyana ndi khamulo, ophunzira ake anamfunsa Iye fanizolo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atalisiya gulu la anthu ndi kulowa mʼnyumba, ophunzira ake anamufunsa za fanizoli
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo m'mene Iye adalowa m'nyumba kusiyana ndi khamulo, ophunzira ace anamfunsa Iye faruzolo.