Mark 7:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo adaaona kuti ophunzira ake ena ankangodya chakudya osasamba m'manja moyenera (ndiye kuti mosasamala mwambo wosamba m'manja.)
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo anaona kuti ophunzira ake ena anadya mkate ndi m'manja mwakuda, ndiwo osasamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
iwo anaona ophunzira ake akudya chakudya ndi mʼmanja mwakuda kapena kuti mʼmanja mosasamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo anaona kuti ophunzira ace ena anadya mkate ndi m'manja mwakuda, ndiwo osasamba.