Mark 7:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa m'kati mwa mitima ya anthu ndiye mumatuluka maganizo oipa, za chiwerewere, za kuba, za kuphana,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti m'kati mwake mwa mitima ya anthu, mutuluka maganizo oipa, zachiwerewere,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti kuchokera mʼkati mwa mitima ya anthu, mumatuluka maganizo oyipa, chiwerewere, kuba, kupha, chigololo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti m'kati mwace mwa mitima ya anthu, muturuka maganizo oipa, zaciwerewere,