Mark 7:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yesu adanyamuka kupita ku dera la ku Tiro. Adakakhala kunyumba kwina, ndipo sadafune kuti anthu adziŵe kuti ali kumeneko. Komabe sadathe kubisika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Iye anauka nachoka kumeneko, nanka ku maiko a ku Tiro ndi Sidoni. Ndipo analowa m'nyumba, nafuna kuti asadziwe anthu; ndipo sanakhoze kubisika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yesu anachoka kumalo amenewo napita ku madera a Turo. Iye analowa mʼnyumba ndipo sanafune wina kuti adziwe zimenezi; komabe sanathe kudzibisa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Iye anauka nacoka kumeneko, nanka ku maiko a ku Turo ndi Sidoni, Ndipo analowa m'nyumba, nafuna kuti asadziwe anthu; ndipo sanakhoza kubisika.