Mark 7:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mai uja adabwerera kunyumba kwake, nakapezadi mwanayo ali gone pa bedi, mzimu woipa uja utatuluka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anachoka kunka kunyumba kwake, napeza mwana atamgoneka pakama, ndi chiwanda chitatuluka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atapita kwawo anakapeza mwana wake aligone pa bedi, chiwanda chitatuluka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anacoka kunka kunyumba kwace, napeza mwana atamgoneka pakama, ndi ciwanda citaturuka.