Mark 7:34 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adayang'ana kumwamba, nadzuma, nkumuuza kuti, “Efata!” ndiye kuti “Tsekuka!”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nagadamira kumwamba, nausa moyo, nanena naye, Efata, ndiko, Tatseguka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anayangʼana kumwamba ndipo ndi mawu otsitsa moyo, anati kwa iye, “Efataa!” (Kutanthauza kuti, “Tsekuka!”)
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nagadamira kumwamba, nausa moyo, nanena naye, Elata, ndiko, Tatseguka.