Mark 7:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono popitiriza mau, Yesu adati, “Koma ndiye muli ndi njira yanu yochenjera yosiyira Malamulo a Mulungu kuti musunge miyambo yanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ananena nao, Bwino mukaniza lamulo la Mulungu, kuti musunge mwambo wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anawawuzanso kuti, “Inu muli ndi njira yabwino yokankhira kumbali malamulo a Mulungu kuti mukatsatire miyambo yanuyo!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ananena nao, Bwino mukaniza lamulo la Mulungu, kuti musunge mwambo wanu,