Mark 8:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pasanapite nthaŵi yaitali anthu ambirimbiri adasonkhananso. Pamene Yesu adaona kuti anthuwo alibe chakudya, adaitana ophunzira ake naŵauza kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Masiku ajawo pakukhalanso khamu lalikulu la anthu, ndipo analibe kanthu kakudya, Iye anadziitanira ophunzira ake, nanena nao,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼmasiku amenewo gulu lina lalikulu la anthu linasonkhana. Popeza iwo analibe chakudya, Yesu anayitana ophunzira ake nati kwa iwo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Masiku ajawo pakukhalanso khamu lalikuru la anthu, ndipo analibe kanthu kakudya, iye anadziitanira ophunzira ace, nanena nao,