Mark 8:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake Yesu adatsazikana nawo anthu aja, kenaka Iye ndi ophunzira ake adaloŵa m'chombo napita ku dera la Dalamanuta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pomwepo analowa m'ngalawa ndi ophunzira ake, nafika ku mbali ya ku Dalamanuta.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
analowa mʼbwato pamodzi ndi ophunzira ake napita ku dera la Dalamanuta.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pomwepo analowa m'ngaiawa ndi akhupunzira ace, nafika ku mbali ya ku Dalmanuta.