Mark 8:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atatero, Yesu adaŵasiya, naloŵanso m'chombo kuwolokera ku tsidya lina.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anawasiya iwo, nalowanso m'ngalawa, nachoka kunka ku tsidya lija.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anawasiya, nalowanso mʼbwato ndi kuwolokera tsidya lina.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anawasiya iwo, nalowanso m'ngalawa, nacoka kunka ku tsidya lija.