Mark 8:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo ophunzirawo adayamba kukambirana nkumati, “Akuterotu chifukwa tilibe buledi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anatsutsana wina ndi mnzake, nanena kuti, Tilibe mikate.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anakambirana wina ndi mnzake ndipo anati, “Ndi chifukwa choti tilibe buledi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anatsutsana wina ndi mnzace, nanena kuti, Tiribe mikate.