Mark 8:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yesu adaŵafunsanso kuti, “Nanga muja ndidaanyemanyema buledi msanu ndi muŵiri ndi kudyetsa anthu zikwi zinaimu, mudaatola madengu angati a zotsala?” Iwo adati, “Madengu asanu ndi aŵiri.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mikate isanu ndi iwiri kwa anthu zikwi zinai, munatola madengu angati odzala ndi makombo? Ndipo ananena naye, Asanu ndi awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ndipo pamene ndinagawa malofu asanu ndi awiri a buledi, kwa anthu 4,000, ndi madengu angati amene munatoleramo buledi ndi nsomba zotsalira?” Iwo anayankha kuti, “Asanu ndi awiri.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mikate isanu ndi iwiri kwa anthu zikwi zinai, munatola malicero angati odzala ndi makombo? Ndipo ananena naye, Asanu ndi awiri.