Mark 9:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo adasungadi chinsinsichi, koma ankafunsana okhaokha kuti, “Kodi kuuka kwa akufa akunena Yesuku ndiye kuti chiyani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anasunga mauwo, nafunsana mwa iwo okha, kuti, Kuuka kwa akufa nchiyani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anayisunga nkhaniyo nakambirana za tanthauzo lake la “Kuuka kwa akufa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anasunga mauwo, nafunsana mwa iwo okha, kuti, Kuuka kwa akufa nciani?