Mark 9:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene anthu onsewo adaona Yesu, adadabwa kwambiri, ndipo adamthamangira kudzamlonjera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pomwepo anthu onse a khamulo, pakumuona Iye, anazizwa kwambiri, namthamangira Iye, namlonjera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nthawi yomweyo anthu onse atamuona, anadabwa kwambiri ndipo anathamanga kukamulonjera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pomwepo anthu onse a khamulo, pakumuona Iye, anazizwa kwambiri, namthamangira Iye, namlankhula.